27/06/2022
1️⃣🌈 *ZINTHU ZOMWE ZIMAYAMBAITSA KUTI ANTHU TIZIDWALA MATENDA YA BP*
👉🏾 ```Kukhala ndithupi kwambiri```
_(Being over weight)_
```👉🏾Nthawi Zina zimatengela ku ntundu wanu ngati kuli ena amadwala BP inuso mumatha kudwa```
_(family history)_
```👉🏾Kukula kuzaka tingoti kukalamba```
_(Older age)_
```👉🏾Kutenga njira zakulela kapena kutseka ubeleki pamene magazi anu Ali a mphamvu kwambiri```
_(birth control)_
```👉🏾Kumangokhala ndinkhawa munthu amatha kuwononga ntima mpakana Kudwala``` *BP*
_(stress)_
```👉🏾Kumamwa mowa mopitilira```
_(alcohol consumption)_
👉🏾 ```Kudya zakudya zamchele kwambiri ndi zina zamafuna anyama```
_(dietary choices/sodium/_ _fats)_
👉🏾 ```Kukhala ndi mimba``` 🤰
_(pregnancy🤰 )_
👉🏾 ```Kudwala matenda ena osiyana siyana monga Diabetes ndi ena akulu akulu amayambitsanso vuto la``` *BP*
_(Chronic condition)_
```👉🏾Kumgwira ntchito malo amodzi yamu office 🏢 monga Kukhala pa computer 🖥 tingoti ntchito zaubwana zosalemetsa zimatha kuyambitsa matenda ya``` *BP*
_(sedentary Works)
*Muzapite kumakheta, amagulisa nyama yambuzi kuja, akakuuzaninso kuti nyamayi or itada chatundu wanji or itagwera pamatope koma sitimasukira ndi sopo ayi, timasukira madzi okha basi*
Ndie azimai ambiri akupwetekeka kumvulala kamba kosukira sopo kundata.
Skin kapena kuti khungu muzisiyanisa ndi ndata, sopo sakuyenera kugunda mkati mwa ndata ayi.
Or kundata kununkhee kwambiri sikoyenera kusukirako sopo ayi koma kusukako ndi madzi okha basi, madzi akenso a warm osati otentha ai.
⬇️Sopo kukuyambisira mauka kundata ndi mwai koma kwambiri amayambisa Cancer ndie pewani.
⬇️Malo ena safunikira kukhuzidwa ndi sopo ndi tisonga tamabele,, tisonga tamabele timakoka pweya choncho ngati watipaka sopo, sopo uja amakokeka kufika mkati zosatira zake azimai amatha kudwala Cancer yamabele *breast cancer* izinso pewani.
↕️Mvuto losapita ku toilet🔽
1️⃣Kukhuta kwambiri ndi zina zomwe zimasokoneza kagaidwe kachakudya mimba, mapeto ake umatenga nthawi usanapite ku toilet.
🔽Munthu umayenera kudya mwa size ndi cholinga choti mimbamo munkhale ndi space yogaya zakudya motakasuka ndimopumira pweya,chifukwa ngati wapakira kwambiri zakudya kupuma ku mamvutirako chifukwa modusa mpweya mumankhala mwapanikizika.
↕️Ndizolakwika zedi Kudya nthawi yomweyo ndikugona pansi, uku kumasokoneza digestion komanso mimba mumawawa, ngati umakonda kugona ukadya.
🍎Chachiwiri nkhazikisani nthawi yanu yomwe muzipita ku toilet,, mimba mumayamba kutentha molingana ndi nthawi yomwe unazizoloweza kupita ku toilet, ngati umapita mazulo ulionse mimbanso mumayamba kukutentha chakumazulo, ngati umapita masana mimbanso mumayamba kukutentha masana.
Ngati mimba mwatentha iwe ndikuzipana osapita ku toilet, ndi zoopsa zedi chifukwa zimasokoneza kagaidwe kachakudya mimba, zosatira zake ukapita ku toilet umalephera kuzithandiza,, and umatenga masiku or week usanapite ku toilet, mimba mumayamba kukupweteka pafupipafupi,, ndie sibwino kuzipana pomwe mimba mwatentha.